v
Aroma 1: 2, Luka 1: 70-71, Machitidwe 3: 20-21, Machitidwe 13: 32-33, Aroma 3: 21-22, Aroma 16: 25-26

Uthengawu unali utanenedweratu kale aneneri a Chipangano Chakale kuti Mwana wa Mulungu abwera kudzatipulumutsa.(Aroma 1: 2, Luka 1:70, Machitidwe 3: 20-21, Machitidwe 13: 32-33)

Khristu wabwera, adalalikirira mwa lamulo ndi Aneneri.Kuti Khristu ndiye Yesu.Chilungamo cha Mulungu chimadza kwa onse okhulupirira Yesu monga Khristu.(Aroma 3: 21-22, Aroma 16: 25-26)